-
Yobu 26:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iye anatambasula kumpoto pamwamba pa malo opanda kanthu,+
Ndipo anakoloweka dziko lapansi m’malere.
-
Salimo 104:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mwadzifunditsa kuwala ngati chofunda,+
Mwatambasula kumwamba ngati nsalu ya chihema.+
-
Yesaya 51:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kodi n’chifukwa chiyani ukuiwala Yehova amene anakupanga,+ amene anatambasula kumwamba+ ndi kuyala maziko a dziko lapansi?+ N’chifukwa chiyani ukuchita mantha nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu, poopa mkwiyo wa yemwe akukupanikizira mkati,+ ngati kuti iye wakonzeka kuti akuwononge?+ Kodi mkwiyo wa amene akukupanikizira mkati uli kuti?+
-
-
-
-
-