Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Iye wokhala kumwamba+ adzaseka,

      Yehova adzawanyodola.+

  • Salimo 29:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Yehova wakhala pampando wake wachifumu pamwamba pa chigumula,*+

      Ndipo Yehova ndi mfumu mpaka kalekale.+

  • Salimo 68:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+

      Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+

  • Yesaya 66:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena