Salimo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu. Salimo 68:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+
4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu.
33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+