Salimo 37:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Yehova adzamuseka,+Pakuti akuona kuti chimaliziro chake chifika.+ Salimo 59:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma inu Yehova, mudzawaseka.+Mudzanyoza mitundu yonse ya anthu.+