1 Samueli 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Davide anapitiriza kunena kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Yehova iye mwini adzamukantha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira mmene amachitira wina aliyense, kapenanso adzapita kunkhondo+ ndipo adzaphedwa kumeneko.+ Yeremiya 50:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iphani ng’ombe zake zonse zazing’ono zamphongo.+ Zonse zipite kokaphedwa.+ Tsoka kwa iwo, chifukwa tsiku lawo lafika. Nthawi yoti alangidwe yafika.+ Ezekieli 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Koma iwe mtsogoleri+ wa Isiraeli, woipa ndi wovulazidwa koopsa,+ nthawi yafika yoti ulangidwe. Mapeto a zolakwa zako afika.+
10 Davide anapitiriza kunena kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Yehova iye mwini adzamukantha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira mmene amachitira wina aliyense, kapenanso adzapita kunkhondo+ ndipo adzaphedwa kumeneko.+
27 Iphani ng’ombe zake zonse zazing’ono zamphongo.+ Zonse zipite kokaphedwa.+ Tsoka kwa iwo, chifukwa tsiku lawo lafika. Nthawi yoti alangidwe yafika.+
25 “Koma iwe mtsogoleri+ wa Isiraeli, woipa ndi wovulazidwa koopsa,+ nthawi yafika yoti ulangidwe. Mapeto a zolakwa zako afika.+