1 Samueli 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nkhondo inam’kulira kwambiri Sauli, moti pamapeto pake oponya mivi ndi uta anamupeza ndipo anamuvulaza koopsa.+ 1 Samueli 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Sauli, ana ake atatu, ndi womunyamulira zida komanso asilikali ake onse, anafera limodzi pa tsiku limenelo.+
3 Nkhondo inam’kulira kwambiri Sauli, moti pamapeto pake oponya mivi ndi uta anamupeza ndipo anamuvulaza koopsa.+
6 Chotero Sauli, ana ake atatu, ndi womunyamulira zida komanso asilikali ake onse, anafera limodzi pa tsiku limenelo.+