2 Samueli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri agwa ndipo afa,+ ngakhalenso Sauli+ ndi mwana wake Yonatani+ afa.” 2 Samueli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mnyamatayo anayankha kuti: “Ndinapezeka kuti ndili paphiri la Giliboa,+ ndipo ndinaona Sauli atatsamira mkondo+ wake. Zili choncho, ndinaona asilikali oyenda m’magaleta ndi asilikali okwera pamahatchi* akumuyandikira.+
4 Kenako Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri agwa ndipo afa,+ ngakhalenso Sauli+ ndi mwana wake Yonatani+ afa.”
6 Mnyamatayo anayankha kuti: “Ndinapezeka kuti ndili paphiri la Giliboa,+ ndipo ndinaona Sauli atatsamira mkondo+ wake. Zili choncho, ndinaona asilikali oyenda m’magaleta ndi asilikali okwera pamahatchi* akumuyandikira.+