Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsiku lotsatira,+ mzimu woipa wochokera kwa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa Sauli,+ moti anayamba kuchita zinthu ngati mneneri+ m’nyumba mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kuimba nyimbo+ ngati kale ndipo Sauli anali ndi mkondo m’manja mwake.+

  • 1 Samueli 19:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno mzimu woipa wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa Sauli ali m’nyumba mwake, atatenga mkondo m’manja mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kumuimbira nyimbo.

  • 1 Samueli 22:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Sauli anamva kuti Davide ndi anthu amene anali naye apezeka. Iye anamva zimenezi ali ku Gibeya pamalo okwezeka, atakhala pansi pa mtengo wa bwemba.+ Sauliyo anali atagwira mkondo+ m’manja mwake ndipo atumiki ake onse anali atamuzungulira.

  • 1 Samueli 26:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero Davide anatenga mkondo ndi mtsuko wa madzi zimene zinali chakumutu kwa Sauli n’kunyamuka. Palibe munthu anawaona+ kapena kuzindikira kalikonse kapenanso kudzuka, pakuti onse anali m’tulo. Tulo timene anagonato tinali tulo tofa nato,+ tochokera kwa Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena