1 Samueli 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsiku lotsatira,+ mzimu woipa wochokera kwa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa Sauli,+ moti anayamba kuchita zinthu ngati mneneri+ m’nyumba mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kuimba nyimbo+ ngati kale ndipo Sauli anali ndi mkondo m’manja mwake.+ 1 Samueli 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno mzimu woipa wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa Sauli ali m’nyumba mwake, atatenga mkondo m’manja mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kumuimbira nyimbo. 1 Samueli 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+
10 Tsiku lotsatira,+ mzimu woipa wochokera kwa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa Sauli,+ moti anayamba kuchita zinthu ngati mneneri+ m’nyumba mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kuimba nyimbo+ ngati kale ndipo Sauli anali ndi mkondo m’manja mwake.+
9 Ndiyeno mzimu woipa wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa Sauli ali m’nyumba mwake, atatenga mkondo m’manja mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kumuimbira nyimbo.
33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+