Genesis 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Motero Yehova Mulungu anagoneka munthuyo tulo tofa nato.+ Munthuyo ali chigonere choncho, Mulungu anamuchotsa nthiti imodzi n’kutseka pamalopo ndi mnofu. Genesis 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Patapita nthawi, dzuwa lili pafupi kulowa, Abulamu anagona tulo tofa nato.+ Pamenepo mdima woopsa wandiweyani unayamba kufika pa iye.
21 Motero Yehova Mulungu anagoneka munthuyo tulo tofa nato.+ Munthuyo ali chigonere choncho, Mulungu anamuchotsa nthiti imodzi n’kutseka pamalopo ndi mnofu.
12 Patapita nthawi, dzuwa lili pafupi kulowa, Abulamu anagona tulo tofa nato.+ Pamenepo mdima woopsa wandiweyani unayamba kufika pa iye.