1 Samueli 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Afilisiti anasonkhana pamodzi ndi kupita kukamanga msasa ku Sunemu.+ Nayenso Sauli anasonkhanitsa Aisiraeli onse pamodzi ndi kumanga msasa ku Giliboa.+ 1 Mbiri 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Afilisiti+ anayamba kumenyana ndi Aisiraeli ndipo amuna a Isiraeli anali kuthawa pamaso pa Afilisitiwo, moti anali kuphedwa m’phiri la Giliboa.+
4 Ndiyeno Afilisiti anasonkhana pamodzi ndi kupita kukamanga msasa ku Sunemu.+ Nayenso Sauli anasonkhanitsa Aisiraeli onse pamodzi ndi kumanga msasa ku Giliboa.+
10 Tsopano Afilisiti+ anayamba kumenyana ndi Aisiraeli ndipo amuna a Isiraeli anali kuthawa pamaso pa Afilisitiwo, moti anali kuphedwa m’phiri la Giliboa.+