Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 20:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno ndidzatumiza mtumiki kuti, ‘Pita ukatole miviyo.’ Koma mtumikiyo ndikadzamuuza mawu akuti, ‘Mivi ili kumbali yakutiyakuti, pita ukatole,’ iweyo ukatuluke chifukwa ndiye kuti zinthu zili bwino ndipo palibe chodetsa nkhawa chilichonse. Ndikulumbira pali Yehova, Mulungu wamoyo.+

  • 1 Samueli 25:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Tsopano mbuyanga, ndikulumbira pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ komanso pali moyo wanu:+ Yehova wakubwezani+ kuti musapalamule mlandu wamagazi+ komanso kuti musadzipulumutse nokha ndi dzanja lanu.+ Choncho lolani kuti adani anu ndi onse ofuna kukuvulazani mbuyanga, akhale ngati Nabala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena