Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+

  • Yesaya 42:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mulungu woona Yehova, amene analenga kumwamba+ ndiponso Wokutambasula Wamkulu,+ amene anakhazikitsa dziko lapansi+ ndi zonse zimene zili mmenemo,+ amene anapereka mpweya+ kwa anthu amene ali mmenemo,+ ndi mzimu kwa anthu amene amayenda padzikopo,+ iye wanena kuti:

  • Yesaya 48:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Komanso dzanja langa linayala maziko a dziko lapansi,+ ndipo dzanja langa lamanja linatambasula kumwamba.+ Ndimafuulira maziko a dziko lapansi ndi kumwamba, kuti ziimirire.+

  • Chivumbulutso 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena