Genesis 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dziko lapansi linali lopanda maonekedwe enieni ndiponso lopanda kanthu. Panali madzi akuya+ kwambiri ndipo pamwamba pake panali mdima wokhawokha. Ndipo mphamvu* ya Mulungu inali kuyendayenda+ pamwamba pa madzi akuyawo.+
2 Dziko lapansi linali lopanda maonekedwe enieni ndiponso lopanda kanthu. Panali madzi akuya+ kwambiri ndipo pamwamba pake panali mdima wokhawokha. Ndipo mphamvu* ya Mulungu inali kuyendayenda+ pamwamba pa madzi akuyawo.+