Genesis 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dziko lapansi linali lopanda chilichonse. Padzikoli panali madzi ambiri+ ndipo pamwamba pake panali mdima wokhawokha. Mphamvu ya Mulungu+ inkayendayenda* pamwamba pa madziwo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 6 Galamukani!,No. 3 2021 tsa. 10 Nsanja ya Olonda,2/15/2007, ptsa. 5-6
2 Dziko lapansi linali lopanda chilichonse. Padzikoli panali madzi ambiri+ ndipo pamwamba pake panali mdima wokhawokha. Mphamvu ya Mulungu+ inkayendayenda* pamwamba pa madziwo.+
1:2 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 6 Galamukani!,No. 3 2021 tsa. 10 Nsanja ya Olonda,2/15/2007, ptsa. 5-6