Yobu 38:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Madzi amadzibisa ngati kuti ali pansi pa mwala,Ndipo pamwamba pa madzi akuya pamauma.+ Miyambo 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene anali kukonza kumwamba, ine ndinali pomwepo.+ Pamene anakhazikitsa lamulo lakuti pamwamba pa madzi akuya pazioneka pozungulira,+
27 Pamene anali kukonza kumwamba, ine ndinali pomwepo.+ Pamene anakhazikitsa lamulo lakuti pamwamba pa madzi akuya pazioneka pozungulira,+