Genesis 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Pa nthawi yoikidwiratu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa. Ndidzabweranso nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.” Yobu 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndadziwa kuti inu mumatha kuchita zinthu zonse,+Ndipo palibe zimene simungakwanitse.+ Luka 1:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Izi zachitika chifukwa zimene Mulungu wanena, sizilephereka.”+ Aroma 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndipo anali wotsimikiza kuti zimene Mulungu analonjeza anali ndi mphamvu yozichita.+
14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Pa nthawi yoikidwiratu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa. Ndidzabweranso nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.”