Salimo 135:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chilichonse chimene Yehova anafuna kuchita anachita.+Anachita zimenezi kumwamba, padziko lapansi, m’nyanja ndi m’madzi onse akuya.+ Yesaya 55:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+
6 Chilichonse chimene Yehova anafuna kuchita anachita.+Anachita zimenezi kumwamba, padziko lapansi, m’nyanja ndi m’madzi onse akuya.+
11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+