Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 135:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Chilichonse chimene Yehova anafuna kuchita anachita.+

      Anachita zimenezi kumwamba, padziko lapansi, m’nyanja ndi m’madzi onse akuya.+

  • Yeremiya 39:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Pita kwa Ebedi-meleki+ Mwitiyopiya ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Taona! Ndikukwaniritsa mawu anga akuti mzinda uwu ndiugwetsera tsoka osati zinthu zabwino.+ Pa tsikulo zimene ndinanena zidzachitika iwe ukuona.”’+

  • Aheberi 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mofanana ndi zimenezi, Mulungu pofuna kuwatsimikizira kwambiri anthu olandira lonjezolo monga cholowa chawo,+ kuti chifuniro chake n’chosasinthika,+ anachita kulumbira pa zimene analonjezazo.

  • Yakobo 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pakuti mwa chifuniro+ chake, iye anatibala ife ndi mawu a choonadi.+ Anachita zimenezi kuti tikhale zipatso zoyambirira+ pa zolengedwa zake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena