Salimo 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+ Salimo 132:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adani ake ndidzawaveka manyazi,+Koma ufumu*+ wake udzapita patsogolo.”+
14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+