Salimo 35:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Onse amene akukondwera ndi tsoka langa,+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Onse odzikweza pamaso panga achite manyazi+ ndi kutsitsidwa.+ Salimo 109:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amene akulimbana ndi ine avale manyazi,+Ndipo adziphimbe ndi manyaziwo ngati akudziphimba ndi malaya akunja odula manja.+
26 Onse amene akukondwera ndi tsoka langa,+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Onse odzikweza pamaso panga achite manyazi+ ndi kutsitsidwa.+
29 Amene akulimbana ndi ine avale manyazi,+Ndipo adziphimbe ndi manyaziwo ngati akudziphimba ndi malaya akunja odula manja.+