Salimo 144:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzaimbira inu amene mumapulumutsa mafumu,+Amene mumalanditsa ine Davide mtumiki wanu ku lupanga lovulaza.+ Miyambo 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Hatchi* anaikonzera tsiku la nkhondo,+ koma Yehova ndiye amapulumutsa.+ Luka 1:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 za kutipulumutsa kwa adani athu ndiponso m’manja mwa onse odana nafe.+
10 Ndidzaimbira inu amene mumapulumutsa mafumu,+Amene mumalanditsa ine Davide mtumiki wanu ku lupanga lovulaza.+