Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iye anaika moyo wake pangozi*+ n’kupha Mfilisiti uja,+ moti Yehova anapereka chipulumutso chachikulu+ kwa Aisiraeli onse. Inuyo munaona zimenezi zikuchitika, ndipo munasangalala. Ndiye n’chifukwa chiyani mukufuna kuchimwira magazi osalakwa, mwa kupha Davide+ popanda chifukwa?”+

  • 2 Samueli 23:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Eleazara ndi amene anaimirira ndipo anali kupha Afilisiti mpaka dzanja lake linatopa, koma anagwirabe lupanga+ moti Yehova anapereka chipulumutso chachikulu pa tsiku limenelo.+ Koma anthu ena onse anamutsatira pambuyo pake kuti avule zovala za anthu ophedwawo.+

  • Salimo 18:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Iye akuchita ntchito zazikulu za chipulumutso kwa mfumu yake,+

      Ndipo akusonyeza kukoma mtima kosatha kwa wodzozedwa wake,+

      kwa Davide ndi mbewu yake mpaka kalekale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena