1 Samueli 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sauli anamvera mawu a Yonatani, ndipo analumbira kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Davide saphedwa.” 1 Samueli 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi yomweyo, Sauli anamulumbirira m’dzina la Yehova kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ sukhala ndi mlandu chifukwa cha nkhani imeneyi!”
6 Sauli anamvera mawu a Yonatani, ndipo analumbira kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Davide saphedwa.”
10 Nthawi yomweyo, Sauli anamulumbirira m’dzina la Yehova kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ sukhala ndi mlandu chifukwa cha nkhani imeneyi!”