1 Samueli 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Samueli anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Inuyo mwachita choipa chachikulu chimenechi. Ngakhale kuti zili choncho, musapatuke n’kusiya kutsatira Yehova,+ koma mutumikire Yehova ndi mtima wanu wonse.+
20 Pamenepo Samueli anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Inuyo mwachita choipa chachikulu chimenechi. Ngakhale kuti zili choncho, musapatuke n’kusiya kutsatira Yehova,+ koma mutumikire Yehova ndi mtima wanu wonse.+