Deuteronomo 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Muzisunga malamulo a Yehova Mulungu wanu mwa kuyenda m’njira zake+ ndi kumuopa.+ Deuteronomo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Tsopano Aisiraeli inu, kodi Yehova Mulungu wanu akufuna kuti muzichita chiyani,+ koposa kuopa+ Yehova Mulungu wanu kuti muziyenda m’njira zake zonse,+ kukonda+ ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+ 1 Atesalonika 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 n’cholinga choti mupitirize kuyenda+ m’njira imene Mulungu, amene akukuitanani+ ku ufumu+ wake ndi ulemerero, amafuna.
12 “Tsopano Aisiraeli inu, kodi Yehova Mulungu wanu akufuna kuti muzichita chiyani,+ koposa kuopa+ Yehova Mulungu wanu kuti muziyenda m’njira zake zonse,+ kukonda+ ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+
12 n’cholinga choti mupitirize kuyenda+ m’njira imene Mulungu, amene akukuitanani+ ku ufumu+ wake ndi ulemerero, amafuna.