Deuteronomo 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Muyende m’njira yonse imene Yehova Mulungu wanu wakulamulani,+ kuti mukhale ndi moyo ndi kuti zinthu zikuyendereni bwino+ ndiponso kuti mutalikitsedi masiku anu m’dziko limene mudzalitenga kukhala lanu. 2 Mbiri 6:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Muchite zimenezi n’cholinga choti iwo akuopeni,+ mwa kuyenda m’njira zanu masiku onse amene angakhale ndi moyo padziko limene munapatsa makolo athu.+ Salimo 128:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 128 Wodala ndi aliyense woopa Yehova,+Amene amayenda m’njira za Mulungu.+ Luka 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Onse awiriwo anali olungama+ pamaso pa Mulungu chifukwa choyenda mokhulupirika,+ mogwirizana ndi malamulo onse+ komanso zofunika za m’chilamulo+ cha Yehova.+
33 Muyende m’njira yonse imene Yehova Mulungu wanu wakulamulani,+ kuti mukhale ndi moyo ndi kuti zinthu zikuyendereni bwino+ ndiponso kuti mutalikitsedi masiku anu m’dziko limene mudzalitenga kukhala lanu.
31 Muchite zimenezi n’cholinga choti iwo akuopeni,+ mwa kuyenda m’njira zanu masiku onse amene angakhale ndi moyo padziko limene munapatsa makolo athu.+
6 Onse awiriwo anali olungama+ pamaso pa Mulungu chifukwa choyenda mokhulupirika,+ mogwirizana ndi malamulo onse+ komanso zofunika za m’chilamulo+ cha Yehova.+