Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Muzisunga malangizo+ ndi zigamulo zake zimene ndikukulamulani lero. Muzitero kuti nthawi zonse zinthu zikuyendereni bwino,+ inuyo ndi ana anu obwera pambuyo panu, ndiponso kuti mutalikitse masiku anu panthaka imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.”+

  • Deuteronomo 12:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “Samala. Uzimvera mawu onsewa amene ndikukuuza,+ kuti zinthu zikuyendere bwino+ mpaka kalekale, iweyo ndi ana ako aamuna obwera m’mbuyo mwako, chifukwa ukatero udzachita chabwino ndi choyenera pamaso pa Yehova Mulungu wako.+

  • Miyambo 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Wosunga lamulo akusunga moyo wake.+ Wosasamala za njira zake adzaphedwa.+

  • Aroma 10:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pajatu Mose analemba kuti munthu wochita chilungamo cha m’Chilamulo adzakhala ndi moyo chifukwa cha chilungamo chimenecho.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena