Levitiko 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno pamene mundawo ukubwezedwa m’Chaka cha Ufulu, uziperekedwa kwa Yehova mpaka kalekale.+ Mundawo ndi wopatulika ndipo uzikhala wa wansembe.+
21 Ndiyeno pamene mundawo ukubwezedwa m’Chaka cha Ufulu, uziperekedwa kwa Yehova mpaka kalekale.+ Mundawo ndi wopatulika ndipo uzikhala wa wansembe.+