Deuteronomo 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “M’munda wako wa mpesa usabzalemo mbewu zamitundu iwiri,+ kuopera kuti ungakakamizike kupereka zokolola zako zonse ndi mphesa zako kumalo opatulika. Ezekieli 44:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwowa ndi amene azidzadya nsembe yambewu, nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.+ Chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mu Isiraeli chidzakhala chawo.+
9 “M’munda wako wa mpesa usabzalemo mbewu zamitundu iwiri,+ kuopera kuti ungakakamizike kupereka zokolola zako zonse ndi mphesa zako kumalo opatulika.
29 Iwowa ndi amene azidzadya nsembe yambewu, nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.+ Chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mu Isiraeli chidzakhala chawo.+