Levitiko 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno pamene mundawo ukubwezedwa m’Chaka cha Ufulu, uziperekedwa kwa Yehova mpaka kalekale.+ Mundawo ndi wopatulika ndipo uzikhala wa wansembe.+ Numeri 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Chinthu chilichonse chimene anthu apatulira Mulungu mu Isiraeli chizikhala chako.+
21 Ndiyeno pamene mundawo ukubwezedwa m’Chaka cha Ufulu, uziperekedwa kwa Yehova mpaka kalekale.+ Mundawo ndi wopatulika ndipo uzikhala wa wansembe.+