3 Ndipo zotsala za nsembe yambewu ndi za Aroni ndi ana ake,+ popeza ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.
18 Mwamuna aliyense+ mwa ana a Aroni azidya mkatewo. Limeneli ndi gawo lawo lochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.+ Chilichonse chimene chingakhudze nsembezi chidzakhala choyera.’”