1 Akorinto 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi simukudziwa kuti anthu ochita ntchito zopatulika amadya+ za m’kachisi, ndipo amene amatumikira+ kuguwa lansembe nthawi zonse amagawana gawo ndi guwa lansembe? 1 Akorinto 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taganizirani zochitika za Isiraeli wakuthupi:+ Kodi amene amadyako zoperekedwa nsembe sindiye kuti akugawana ndi guwa lansembe?+
13 Kodi simukudziwa kuti anthu ochita ntchito zopatulika amadya+ za m’kachisi, ndipo amene amatumikira+ kuguwa lansembe nthawi zonse amagawana gawo ndi guwa lansembe?
18 Taganizirani zochitika za Isiraeli wakuthupi:+ Kodi amene amadyako zoperekedwa nsembe sindiye kuti akugawana ndi guwa lansembe?+