-
Numeri 36:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Cholowa cha ana a Isiraeli chisachoke ku fuko lina kupita ku fuko lina. Aliyense wa ana a Isiraeli ayenera kusunga cholowa cha fuko la makolo ake.
-