2 Mbiri 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ineyo ndidzakuchotsani padziko langa limene ndakupatsani+ ndipo nyumba iyi yomwe ndaiyeretsa+ chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Ndidzachititsa anthu kuipekera mwambi+ ndi kuitonza pakati pa mitundu yonse ya anthu.+ Salimo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+ Salimo 85:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 85 Inu Yehova, mwasangalala ndi dziko lanu.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+ Yoweli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yehova adzachitira nsanje dziko lake+ ndipo adzamvera chifundo anthu ake.+
20 ineyo ndidzakuchotsani padziko langa limene ndakupatsani+ ndipo nyumba iyi yomwe ndaiyeretsa+ chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Ndidzachititsa anthu kuipekera mwambi+ ndi kuitonza pakati pa mitundu yonse ya anthu.+
24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+
85 Inu Yehova, mwasangalala ndi dziko lanu.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+