1 Mbiri 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala m’dziko la eni+ monga analili makolo athu onse. Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi,+ ndipo ndife osakhalitsa. Salimo 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,Ndipo tcherani khutu pamene ndikufuula kupempha thandizo.+Musandinyalanyaze pamene ndikugwetsa misozi.+Pakuti ndine mlendo wanu,+Mlendo wokhala nanu monga anachitira makolo anga onse.+ 1 Petulo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa m’dzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa zilakolako za thupi+ zimene zili pa nkhondo yolimbana ndi moyo.+
15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala m’dziko la eni+ monga analili makolo athu onse. Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi,+ ndipo ndife osakhalitsa.
12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,Ndipo tcherani khutu pamene ndikufuula kupempha thandizo.+Musandinyalanyaze pamene ndikugwetsa misozi.+Pakuti ndine mlendo wanu,+Mlendo wokhala nanu monga anachitira makolo anga onse.+
11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa m’dzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa zilakolako za thupi+ zimene zili pa nkhondo yolimbana ndi moyo.+