Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 27:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Amenewa ndiwo malamulo+ amene Yehova anapatsa Mose paphiri la Sinai+ kuti apereke kwa ana a Isiraeli.

  • Numeri 36:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Amenewa ndiwo malamulo+ ndi zigamulo za Yehova, zimene anapereka kwa ana a Isiraeli kudzera kwa Mose ku Yeriko, m’chipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano.+

  • Salimo 19:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+

      Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+

  • Salimo 119:151
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 151 Inu Yehova muli pafupi,+

      Ndipo malamulo anu onse ndi choonadi.+

  • Mlaliki 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena