Deuteronomo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse? Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+ Salimo 145:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ali pafupi ndi onse oitanira pa iye.+Iye ali pafupi ndi onse amene amamuitana m’choonadi,+
7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse?
46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+