Ekisodo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo mundipangire malo opatulika, popeza ndiyenera kukhala pakati panu.+ Levitiko 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Motero ndidzayendadi pakati panu ndi kukusonyezani kuti ine ndine Mulungu wanu,+ ndipo inu mudzakhala anthu anga.+ Deuteronomo 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti ndani mwa anthu onse amene anamvetserapo mawu a Mulungu wamoyo,+ akulankhula kuchokera pakati pa moto monga mmene tachitira ife n’kukhalabe ndi moyo? Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+ Salimo 145:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ali pafupi ndi onse oitanira pa iye.+Iye ali pafupi ndi onse amene amamuitana m’choonadi,+
12 Motero ndidzayendadi pakati panu ndi kukusonyezani kuti ine ndine Mulungu wanu,+ ndipo inu mudzakhala anthu anga.+
26 Pakuti ndani mwa anthu onse amene anamvetserapo mawu a Mulungu wamoyo,+ akulankhula kuchokera pakati pa moto monga mmene tachitira ife n’kukhalabe ndi moyo?
46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+