Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse?

  • 1 Mafumu 18:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Pa nthawi+ yopereka nsembe yambewu, Eliya mneneri anayandikira guwa lansembelo n’kunena kuti: “Inu Yehova Mulungu wa Abulahamu,+ Isaki,+ ndi Isiraeli,+ lero zidziwike kuti inu ndinu Mulungu mu Isiraeli,+ ndi kuti ine ndine mtumiki wanu, komanso kuti ndachita zonsezi potsatira mawu anu.+

  • Salimo 34:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Yehova ali pafupi ndi anthu a mtima wosweka.+

      Ndipo odzimvera chisoni mumtima mwawo amawapulumutsa.+

  • Yakobo 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yandikirani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu,+ okayikakayika inu.+

  • Yuda 24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Koma ponena za Mulungu amene angathe kukutetezani+ kuti musapunthwe, ndiponso kukuikani opanda chilema+ pamaso pa ulemerero wake ndi chisangalalo chachikulu,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena