Numeri 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Mose anati: “Mudziwira izi kuti Yehova ndiye anandituma kuti ndichite zonsezi,+ ndiponso kuti si za mumtima mwanga ayi:+ 2 Samueli 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu mwachita zazikulu zonsezi monga mwa mawu anu,+ komanso mogwirizana ndi zofuna za mtima wanu,+ ndipo mwandidziwitsa ine mtumiki wanu.+ Yohane 11:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Inde, ndikudziwa kuti mumandimva nthawi zonse, koma ndikunena izi chifukwa cha khamu la anthu+ aimirira panowa, kuti akhulupirire kuti inu munandituma ine.”+
28 Ndiyeno Mose anati: “Mudziwira izi kuti Yehova ndiye anandituma kuti ndichite zonsezi,+ ndiponso kuti si za mumtima mwanga ayi:+
21 Inu mwachita zazikulu zonsezi monga mwa mawu anu,+ komanso mogwirizana ndi zofuna za mtima wanu,+ ndipo mwandidziwitsa ine mtumiki wanu.+
42 Inde, ndikudziwa kuti mumandimva nthawi zonse, koma ndikunena izi chifukwa cha khamu la anthu+ aimirira panowa, kuti akhulupirire kuti inu munandituma ine.”+