Ekisodo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Mulungu anati: “Chifukwa ndidzakhala nawe.+ Ndipo chizindikiro chako chakuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi:+ Pambuyo powatulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira Mulungu woona paphiri lino.”+ Deuteronomo 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mneneri akalankhula m’dzina la Yehova, koma mawuwo sanachitike kapena kukwaniritsidwa, ndiye kuti si Yehova amene walankhula mawu amenewo.+ Mneneriyo walankhula mawu amenewo mwa iye yekha, modzikuza. Iwe usachite naye mantha.’+ Yohane 5:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma ine ndili ndi umboni woposa wa Yohane, pakuti ntchito zenizenizo zimene Atate wanga anandipatsa kuti ndizikwaniritse, ntchito zimene ine ndikuchita,+ zikundichitira umboni kuti Atate ananditumadi.
12 Pamenepo Mulungu anati: “Chifukwa ndidzakhala nawe.+ Ndipo chizindikiro chako chakuti ine ndi amene ndakutuma ndi ichi:+ Pambuyo powatulutsa anthuwo mu Iguputo, anthu inu mudzatumikira Mulungu woona paphiri lino.”+
22 Mneneri akalankhula m’dzina la Yehova, koma mawuwo sanachitike kapena kukwaniritsidwa, ndiye kuti si Yehova amene walankhula mawu amenewo.+ Mneneriyo walankhula mawu amenewo mwa iye yekha, modzikuza. Iwe usachite naye mantha.’+
36 Koma ine ndili ndi umboni woposa wa Yohane, pakuti ntchito zenizenizo zimene Atate wanga anandipatsa kuti ndizikwaniritse, ntchito zimene ine ndikuchita,+ zikundichitira umboni kuti Atate ananditumadi.