Yohane 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yesu anawauza kuti: “Ntchito ya Mulungu ndi iyi, musonyeze chikhulupiriro+ mwa amene Iyeyo anamutuma.”+ Yohane 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 chifukwa mawu amene munandipatsa ndawapereka kwa iwo.+ Iwo awalandira ndipo adziwa ndithu kuti ine ndinabwera monga nthumwi yanu,+ ndipo akhulupirira kuti ndinu amene munandituma.+
29 Yesu anawauza kuti: “Ntchito ya Mulungu ndi iyi, musonyeze chikhulupiriro+ mwa amene Iyeyo anamutuma.”+
8 chifukwa mawu amene munandipatsa ndawapereka kwa iwo.+ Iwo awalandira ndipo adziwa ndithu kuti ine ndinabwera monga nthumwi yanu,+ ndipo akhulupirira kuti ndinu amene munandituma.+