Salimo 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+ Amosi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+
14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+