1 Mbiri 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu Yehova, chifukwa cha ine mtumiki wanu, komanso mogwirizana ndi zofuna za mtima wanu,+ mwachita zazikulu zonsezi mwa kundidziwitsa zinthu zonse zazikulu zimene mudzachita.+
19 Inu Yehova, chifukwa cha ine mtumiki wanu, komanso mogwirizana ndi zofuna za mtima wanu,+ mwachita zazikulu zonsezi mwa kundidziwitsa zinthu zonse zazikulu zimene mudzachita.+