2 Samueli 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu mwachita zazikulu zonsezi monga mwa mawu anu,+ komanso mogwirizana ndi zofuna za mtima wanu,+ ndipo mwandidziwitsa ine mtumiki wanu.+ Salimo 135:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chilichonse chimene Yehova anafuna kuchita anachita.+Anachita zimenezi kumwamba, padziko lapansi, m’nyanja ndi m’madzi onse akuya.+
21 Inu mwachita zazikulu zonsezi monga mwa mawu anu,+ komanso mogwirizana ndi zofuna za mtima wanu,+ ndipo mwandidziwitsa ine mtumiki wanu.+
6 Chilichonse chimene Yehova anafuna kuchita anachita.+Anachita zimenezi kumwamba, padziko lapansi, m’nyanja ndi m’madzi onse akuya.+