1 Mbiri 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu Yehova Mulungu wa Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli makolo athu,+ thandizani anthu awa kuti apitirizebe kukhala ndi mtima wodzipereka woterewu,+ ndiponso kuti akutumikireni ndi mtima wawo wonse.+ Mateyu 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo’?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+
18 Inu Yehova Mulungu wa Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli makolo athu,+ thandizani anthu awa kuti apitirizebe kukhala ndi mtima wodzipereka woterewu,+ ndiponso kuti akutumikireni ndi mtima wawo wonse.+
32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo’?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+