Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 28:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamwamba pa makwererowo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti:+

      “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako, ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+

  • Genesis 31:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Atiweruze mulungu wa Abulahamu,+ mulungu wa Nahori,+ yemwe ali mulungu wa bambo awo.” Koma Yakobo analumbira pa Mulungu amene bambo ake Isaki anali kumuopa.+

  • Genesis 32:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Atatero, Yakobo anati: “Mulungu wa kholo langa Abulahamu, Mulungu wa bambo anga Isaki,+ inu Yehova munandiuza kuti, ‘Bwerera kudziko lakwanu, kwa abale ako, ndipo ndidzakusamalira.’+

  • Genesis 46:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mulungu anapitiriza kuti: “Ine ndine Mulungu woona,+ Mulungu wa bambo ako.+ Usaope kupita ku Iguputo, chifukwa kumeneko ndidzakukuza kukhala mtundu waukulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena