Genesis 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usiku umenewo, Yehova anaonekera kwa iye ndipo anamuuza kuti: “Ine ndine Mulungu wa Abulahamu bambo ako.+ Usaope,+ chifukwa ndili nawe. Ndidzakudalitsa ndi kuchulukitsa mbewu yako chifukwa cha Abulahamu mtumiki wanga.”+ 2 Mbiri 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi inuyo Mulungu wathu+ si paja munathamangitsa anthu amene anali kukhala m’dziko lino pamaso pa anthu anu Aisiraeli,+ n’kulipereka+ kwa mbewu ya Abulahamu yemwe anali kukukondani,+ kuti likhale lawo mpaka kalekale?
24 Usiku umenewo, Yehova anaonekera kwa iye ndipo anamuuza kuti: “Ine ndine Mulungu wa Abulahamu bambo ako.+ Usaope,+ chifukwa ndili nawe. Ndidzakudalitsa ndi kuchulukitsa mbewu yako chifukwa cha Abulahamu mtumiki wanga.”+
7 Kodi inuyo Mulungu wathu+ si paja munathamangitsa anthu amene anali kukhala m’dziko lino pamaso pa anthu anu Aisiraeli,+ n’kulipereka+ kwa mbewu ya Abulahamu yemwe anali kukukondani,+ kuti likhale lawo mpaka kalekale?