Yeremiya 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+ Ezekieli 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kuti azidzatsatira malamulo anga, azidzasunga zigamulo zanga ndi kuzikwaniritsa.+ Iwo adzakhaladi anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”’+
23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+
20 kuti azidzatsatira malamulo anga, azidzasunga zigamulo zanga ndi kuzikwaniritsa.+ Iwo adzakhaladi anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”’+